Oweruza 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ali mkati mosangalala, amuna opanda pake amumzindawo, anazungulira nyumbayo nʼkuyamba kumenya chitseko. Iwo ankauza bambo wachikulireyo, mwiniwake wa nyumbayo, kuti: “Tulutsa mwamuna amene wabwera mʼnyumba yako kuti tigone naye.”+
22 Ali mkati mosangalala, amuna opanda pake amumzindawo, anazungulira nyumbayo nʼkuyamba kumenya chitseko. Iwo ankauza bambo wachikulireyo, mwiniwake wa nyumbayo, kuti: “Tulutsa mwamuna amene wabwera mʼnyumba yako kuti tigone naye.”+