-
Oweruza 19:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mwini nyumbayo anatuluka nʼkuwauza kuti: “Ayi abale anga, musachite zoipa zimenezo, chifukwatu munthuyu ndi mlendo wanga. Musachite zinthu zochititsa manyazi chonchi.
-