Oweruza 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndili ndi mwana wamkazi amene ndi namwali ndiponso pali wantchito wamkazi wa mwamunayu. Bwanji ndikutulutsireni amenewa kuti muwachite chipongwe chimene mukufunacho?+ Koma mwamunayu musamʼchitire zinthu zochititsa manyazi ngati zimenezo.”
24 Ndili ndi mwana wamkazi amene ndi namwali ndiponso pali wantchito wamkazi wa mwamunayu. Bwanji ndikutulutsireni amenewa kuti muwachite chipongwe chimene mukufunacho?+ Koma mwamunayu musamʼchitire zinthu zochititsa manyazi ngati zimenezo.”