Oweruza 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma anthuwo sanamumvere, moti Mleviyo anatenga mkazi wakeyo+ nʼkumupereka kwa anthuwo. Anthuwo anayamba kumugwiririra ndiponso kumuzunza usiku wonse mpaka mʼbandakucha. Kenako kutayamba kucha anamusiya kuti azipita.
25 Koma anthuwo sanamumvere, moti Mleviyo anatenga mkazi wakeyo+ nʼkumupereka kwa anthuwo. Anthuwo anayamba kumugwiririra ndiponso kumuzunza usiku wonse mpaka mʼbandakucha. Kenako kutayamba kucha anamusiya kuti azipita.