-
Oweruza 19:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mbuye wake atadzuka mʼmawa nʼkutsegula zitseko za nyumbayo, kuti apitirize ulendo wake, anaona mkazi uja atagona panja pa nyumbayo manja ake ali pakhomo.
-