-
Oweruza 19:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndiyeno anauza mkaziyo kuti: “Dzuka tizipita.” Koma sanayankhe. Zitatero, anamukweza pabulu nʼkumapita.