Oweruza 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mlevi uja,+ mwamuna wake wa mkazi wophedwa uja, anayankha kuti: “Ine ndi mkazi wanga tinafika ku Gibeya,+ mʼdera la Benjamini, kuti tigone kumeneko.
4 Mlevi uja,+ mwamuna wake wa mkazi wophedwa uja, anayankha kuti: “Ine ndi mkazi wanga tinafika ku Gibeya,+ mʼdera la Benjamini, kuti tigone kumeneko.