Oweruza 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu* a ku Gibeya anabwera usiku nʼkuzungulira nyumba imene ndinagona. Iwo ankafuna kundipha, koma mʼmalomwake anagwirira mkazi wanga mpaka anafa.+
5 Ndiyeno anthu* a ku Gibeya anabwera usiku nʼkuzungulira nyumba imene ndinagona. Iwo ankafuna kundipha, koma mʼmalomwake anagwirira mkazi wanga mpaka anafa.+