-
Oweruza 20:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno mafuko a Isiraeli anatumiza amuna kwa atsogoleri onse a fuko la Benjamini, kukawafunsa kuti: “Kodi zinthu zoipazi, zomwe zachitika mumzinda wanu, zachitika chifukwa chiyani?
-