Oweruza 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyetu bweretsani anthu opanda pake a mu Gibeyawo+ kuti tiwaphe nʼkuchotsa choipachi mu Isiraeli.”+ Koma anthu a fuko la Benjamini anakana kumvera zimene Aisiraeli anzawowo ananena.
13 Ndiyetu bweretsani anthu opanda pake a mu Gibeyawo+ kuti tiwaphe nʼkuchotsa choipachi mu Isiraeli.”+ Koma anthu a fuko la Benjamini anakana kumvera zimene Aisiraeli anzawowo ananena.