-
Oweruza 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndiyeno anthu a fuko la Benjamini ananyamuka mʼmizinda yawo nʼkukasonkhana ku Gibeya kuti akamenyane ndi amuna a ku Isiraeli.
-