Oweruza 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna a ku Isiraeli okhala ndi malupanga amene anasonkhanitsidwa analipo 400,000,+ osawerengera amuna amʼdera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali msilikali wodziwa kumenya nkhondo.
17 Amuna a ku Isiraeli okhala ndi malupanga amene anasonkhanitsidwa analipo 400,000,+ osawerengera amuna amʼdera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali msilikali wodziwa kumenya nkhondo.