-
Oweruza 20:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Zitatero, anthu a fuko la Benjamini anatuluka mumzinda wa Gibeya nʼkupha amuna a Isiraeli 22,000 tsiku limenelo.
-