-
Oweruza 20:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma asilikali a Isiraeli analimba mtima ndipo anapitanso kukaima pamalo omwe aja pokonzekera kumenya nkhondo ngati mmene anachitira tsiku loyamba lija.
-