Oweruza 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero anthu a fuko la Benjamini anatuluka mumzinda wa Gibeya kudzakumana nawo tsiku lachiwirilo, ndipo anaphanso Aisiraeli 18,000.+ Onse amene anaphedwawo anali amuna okhala ndi malupanga.
25 Zitatero anthu a fuko la Benjamini anatuluka mumzinda wa Gibeya kudzakumana nawo tsiku lachiwirilo, ndipo anaphanso Aisiraeli 18,000.+ Onse amene anaphedwawo anali amuna okhala ndi malupanga.