Oweruza 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova anagonjetsa anthu a fuko la Benjamini+ pamaso pa Aisiraeli, moti tsiku limeneli Aisiraeli anapha anthu a fuko la Benjamini 25,100. Onsewa anali amuna okhala ndi malupanga.+
35 Yehova anagonjetsa anthu a fuko la Benjamini+ pamaso pa Aisiraeli, moti tsiku limeneli Aisiraeli anapha anthu a fuko la Benjamini 25,100. Onsewa anali amuna okhala ndi malupanga.+