-
Oweruza 20:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Iwo anazungulira anthu a fuko la Benjamini ndipo anawathamangitsa osawasiya moti anawagonjetsera pafupi penipeni ndi mzimda wa Gibeya, chakumʼmawa.
-