Oweruza 20:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pamapeto pake, amuna 18,000 a fuko la Benjamini anaphedwa ndipo onsewa anali asilikali amphamvu.+