-
Oweruza 20:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Amuna a Isiraeli anabwerera kukapha ndi lupanga anthu a fuko la Benjamini amene anatsala mumzinda komanso ziweto. Anapha chilichonse chimene anapeza. Kuwonjezera apo, anayatsa moto mizinda yonse imene ankaipeza mʼnjira.
-