-
Oweruza 21:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Aisiraeli anati: “Pa mafuko onse a Isiraeli ndi ndani sanabwere kudzasonkhana pamaso pa Yehova?” Popeza anali atalumbira kuti aliyense amene sabwera kwa Yehova ku Mizipa, aphedwe ndithu.
-