Oweruza 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kufunsana kuti: “Pa mafuko onse a Isiraeli ndi ndani sanabwere pamaso pa Yehova ku Mizipa?”+ Ndiyeno anaona kuti panalibe aliyense wochokera ku Yabesi-giliyadi amene anabwera kumsasa kumene kunali mpingowo.
8 Anayamba kufunsana kuti: “Pa mafuko onse a Isiraeli ndi ndani sanabwere pamaso pa Yehova ku Mizipa?”+ Ndiyeno anaona kuti panalibe aliyense wochokera ku Yabesi-giliyadi amene anabwera kumsasa kumene kunali mpingowo.