Oweruza 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho gulu la Aisiraelilo linatumiza amuna amphamvu kwambiri okwana 12,000. Anawalamula kuti: “Pitani, mukaphe ndi lupanga anthu a ku Yabesi-giliyadi ndipo mukaphenso akazi ndi ana omwe.+
10 Choncho gulu la Aisiraelilo linatumiza amuna amphamvu kwambiri okwana 12,000. Anawalamula kuti: “Pitani, mukaphe ndi lupanga anthu a ku Yabesi-giliyadi ndipo mukaphenso akazi ndi ana omwe.+