-
Oweruza 21:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno mukakaona atsikana a ku Silo akubwera kudzavina magule awo ovina mozungulira, aliyense akatuluke mʼminda ya mpesayo, nʼkugwira mtsikana pakati pa atsikana a ku Silo, ndipo akapite naye kudera la Benjamini kuti akakhale mkazi wake.
-