Oweruza 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anthu a fuko la Benjamini anachitadi zimenezo. Ndipo aliyense anatenga mkazi pa akazi amene ankavina. Atatero, anabwerera kumalo awo ndipo anamanganso mizinda+ ija nʼkumakhalamo.
23 Choncho anthu a fuko la Benjamini anachitadi zimenezo. Ndipo aliyense anatenga mkazi pa akazi amene ankavina. Atatero, anabwerera kumalo awo ndipo anamanganso mizinda+ ija nʼkumakhalamo.