Rute 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tsopano, pa nthawi imene oweruza+ ankatsogolera* ku Isiraeli, mʼdzikomo munagwa njala. Ndiyeno munthu wina anasamuka ku Betelehemu+ wa ku Yuda nʼkukakhala ngati mlendo ku Mowabu.+ Anasamuka ndi mkazi wake ndi ana ake awiri aamuna. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Tsanzirani, ptsa. 33-35 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, tsa. 23
1 Tsopano, pa nthawi imene oweruza+ ankatsogolera* ku Isiraeli, mʼdzikomo munagwa njala. Ndiyeno munthu wina anasamuka ku Betelehemu+ wa ku Yuda nʼkukakhala ngati mlendo ku Mowabu.+ Anasamuka ndi mkazi wake ndi ana ake awiri aamuna.