Rute 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthuyu dzina lake anali Elimeleki,* ndipo mkazi wake anali Naomi.* Mayina a ana akewo anali Maloni* ndi Kiliyoni.* Anthuwa anali a ku Betelehemu Efurata wa ku Yuda. Ndipo anafika ku Mowabu nʼkumakhala kumeneko.
2 Munthuyu dzina lake anali Elimeleki,* ndipo mkazi wake anali Naomi.* Mayina a ana akewo anali Maloni* ndi Kiliyoni.* Anthuwa anali a ku Betelehemu Efurata wa ku Yuda. Ndipo anafika ku Mowabu nʼkumakhala kumeneko.