Rute 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawo anakwatira akazi a Chimowabu. Wina dzina lake anali Olipa ndipo wina anali Rute.+ Iwo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Tsanzirani, tsa. 35 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, ptsa. 23-24
4 Kenako anawo anakwatira akazi a Chimowabu. Wina dzina lake anali Olipa ndipo wina anali Rute.+ Iwo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.