Rute 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Naomi anati: “Bwererani ana anga. Palibe chifukwa choti tipitire limodzi. Kodi ndingathe kuberekanso ana amene angadzakhale amuna anu?+
11 Koma Naomi anati: “Bwererani ana anga. Palibe chifukwa choti tipitire limodzi. Kodi ndingathe kuberekanso ana amene angadzakhale amuna anu?+