Rute 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kodi mungawadikire mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwanso kuti mudzakwatiwe ndi iwowo? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, chifukwa dzanja la Yehova landiukira.”+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2021, ptsa. 9-10 Nsanja ya Olonda,3/1/2005, tsa. 27
13 kodi mungawadikire mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwanso kuti mudzakwatiwe ndi iwowo? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, chifukwa dzanja la Yehova landiukira.”+