-
Rute 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri ngati chinachake kupatulapo imfa chingandisiyanitse ndi inu.”
-