Rute 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anapitiriza ulendo wawo mpaka anafika ku Betelehemu.+ Atangofika ku Betelehemu, mumzinda wonsewo anthu anayamba kulankhula za iwo. Azimayi ankafunsa kuti: “Kodi si Naomi uyu?” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Tsanzirani, ptsa. 38-39 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, ptsa. 26-27
19 Ndipo anapitiriza ulendo wawo mpaka anafika ku Betelehemu.+ Atangofika ku Betelehemu, mumzinda wonsewo anthu anayamba kulankhula za iwo. Azimayi ankafunsa kuti: “Kodi si Naomi uyu?”