Rute 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Panali munthu wina wolemera kwambiri yemwe anali wachibale wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi+ ndipo anali wa kubanja la Elimeleki.
2 Panali munthu wina wolemera kwambiri yemwe anali wachibale wa mwamuna wake wa Naomi. Dzina lake anali Boazi+ ndipo anali wa kubanja la Elimeleki.