Rute 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zitatero Rute ananyamuka nʼkupita ndipo anakalowa mʼmunda wina nʼkuyamba kukunkha pambuyo pa anthu okolola. Ndiye zinangochitika kuti mundawo unali wa Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.+
3 Zitatero Rute ananyamuka nʼkupita ndipo anakalowa mʼmunda wina nʼkuyamba kukunkha pambuyo pa anthu okolola. Ndiye zinangochitika kuti mundawo unali wa Boazi,+ wa kubanja la Elimeleki.+