Rute 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzingoyangʼana mbali imene akukolola ndipo uziwatsatira. Anyamatawa ndawalamula kuti asakuvutitse.* Ukamva ludzu, uzipita kukamwa madzi amene ali mʼmitsukoyo, omwe anyamatawa atunga.” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 5
9 Uzingoyangʼana mbali imene akukolola ndipo uziwatsatira. Anyamatawa ndawalamula kuti asakuvutitse.* Ukamva ludzu, uzipita kukamwa madzi amene ali mʼmitsukoyo, omwe anyamatawa atunga.”