Rute 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, nʼkunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chonchi, ine wokhala mlendo?”+
10 Atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, nʼkunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mundiganizire ndi kundikomera mtima chonchi, ine wokhala mlendo?”+