-
Rute 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Rute atamva zimenezi anati: “Mwandikomera mtima mbuyanga. Mwandilimbikitsa komanso mwalankhula mondilimbitsa mtima ngakhale kuti si ine mmodzi wa antchito anu.”
-