Rute 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatha kudya ananyamuka nʼkukayambanso kukunkha.+ Boazi analamula anyamata ake kuti: “Muzimulola kukunkha barele* ndipo musamʼvutitse.+
15 Atatha kudya ananyamuka nʼkukayambanso kukunkha.+ Boazi analamula anyamata ake kuti: “Muzimulola kukunkha barele* ndipo musamʼvutitse.+