Rute 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Rute anapitiriza kukunkha mʼmundamo mpaka madzulo.+ Atamaliza kumenya balere amene anakunkhayo anakwana pafupifupi muyezo umodzi wa efa.* Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Tsanzirani, ptsa. 42-43 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, ptsa. 19-20
17 Choncho Rute anapitiriza kukunkha mʼmundamo mpaka madzulo.+ Atamaliza kumenya balere amene anakunkhayo anakwana pafupifupi muyezo umodzi wa efa.*