Rute 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano apongozi ake anamʼfunsa kuti: “Kodi lero unakakunkha kuti? Adalitsike amene wakuganizirayo.”+ Ndiyeno iye anauza apongozi akewo za munda umene anakakunkhamo. Anawauza kuti: “Munda umene ndakunkhamo lero, eniake ndi a Boazi.” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Tsanzirani, tsa. 43 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 20
19 Tsopano apongozi ake anamʼfunsa kuti: “Kodi lero unakakunkha kuti? Adalitsike amene wakuganizirayo.”+ Ndiyeno iye anauza apongozi akewo za munda umene anakakunkhamo. Anawauza kuti: “Munda umene ndakunkhamo lero, eniake ndi a Boazi.”