Rute 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Rute mkazi wa Chimowabuyo anati: “Moti anandiuzanso kuti, ‘Usachoke, uzikhala pafupi ndi antchito angawa mpaka adzamalize kukolola.’”+
21 Ndiyeno Rute mkazi wa Chimowabuyo anati: “Moti anandiuzanso kuti, ‘Usachoke, uzikhala pafupi ndi antchito angawa mpaka adzamalize kukolola.’”+