-
Rute 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Naomi anauza Rute mpongozi wakeyo kuti: “Zingakhale bwinodi mwana wanga, uzipita limodzi ndi atsikana akewo, kusiyana nʼkuti akakuchite chipongwe kumunda wina.”
-