Rute 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pajatu Boazi ndi wachibale wathu.+ Ndipo atsikana ake antchito wakhala ukugwira nawo ntchito. Usiku walero iye akhala akupeta balere pamalo ake opunthira.
2 Pajatu Boazi ndi wachibale wathu.+ Ndipo atsikana ake antchito wakhala ukugwira nawo ntchito. Usiku walero iye akhala akupeta balere pamalo ake opunthira.