-
Rute 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno akamakagona, ukaone kuti wagona pati. Kenako ukapite pamene wagonapo ndipo ukamuvundukule mapazi nʼkugona pomwepo. Iye akakuuza zochita.”
-