-
Rute 3:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho anagonabe kumapazi a Boazi mpaka mʼmamawa. Kenako anadzuka kudakali mdima chifukwa Boazi sanafune kuti anthu adziwe kuti kopunthira mbewuko kunabwera mkazi.
-