Rute 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno anamuuza kuti: “Bweretsa nsalu wafundayo ndipo uitambasule.” Iye anaitambasuladi ndipo Boazi anathirapo miyezo 6* ya balere nʼkumusenza pamutu. Kenako Boazi analowa mumzinda. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Tsanzirani, tsa. 48 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 233/1/2005, tsa. 29
15 Ndiyeno anamuuza kuti: “Bweretsa nsalu wafundayo ndipo uitambasule.” Iye anaitambasuladi ndipo Boazi anathirapo miyezo 6* ya balere nʼkumusenza pamutu. Kenako Boazi analowa mumzinda.