Rute 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Rute anabwerera kwa apongozi ake, ndipo iwo anamufunsa kuti: “Wayendako bwanji* mwana wanga?” Iye anawafotokozera zonse zimene Boazi anamuchitira. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Tsanzirani, tsa. 48 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 233/1/2005, tsa. 29
16 Tsopano Rute anabwerera kwa apongozi ake, ndipo iwo anamufunsa kuti: “Wayendako bwanji* mwana wanga?” Iye anawafotokozera zonse zimene Boazi anamuchitira.