-
Rute 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Atatero, Naomi anayankha kuti: “Tiye tingodikira mwana wanga, mpaka utadziwa mmene nkhaniyi ithere. Chifukwa iye sakhala pansi mpaka ataithetsa nkhaniyi lero.”
-