Rute 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndikutenga Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira libwerere pacholowa chake+ komanso kuti lisafafanizidwe pakati pa abale ake ndiponso mumzindawu. Inu ndinu mboni lero.”+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:10 Tsanzirani, tsa. 50 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 24
10 Komanso ndikutenga Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira libwerere pacholowa chake+ komanso kuti lisafafanizidwe pakati pa abale ake ndiponso mumzindawu. Inu ndinu mboni lero.”+