-
Rute 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zitatero azimayi anayamba kuuza Naomi kuti: “Atamandike Yehova, amene wachititsa kuti upeze wokuwombola lero. Dzina lake lifalitsidwe mu Isiraeli.
-