1 Samueli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Hana anamʼpatsa gawo lapadera chifukwa ndi amene ankamukonda, komabe Yehova sanamupatse ana.* 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Tsanzirani, tsa. 52 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, tsa. 15